-
Levitiko 19:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Ndiyeno wansembe aziphimba tchimo limene munthuyo wachita. Azichita zimenezi popereka kwa Yehova nkhosa yamphongo ya nsembe yakupalamula ija ndipo munthuyo adzakhululukidwa tchimo lakelo.
-