-
Levitiko 19:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Mukafika mʼdziko limene mukupita nʼkudzala mtengo uliwonse wa zipatso, zipatso zake zizikhala zodetsedwa kwa inu ndipo mtengowo musamauyandikire. Musamayandikire mtengowo kwa zaka zitatu ndipo musamadye zipatso zake.
-