Levitiko 19:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Musamanyoze mwana wanu wamkazi pomupangitsa kuti akhale hule,+ kuopera kuti dziko lingachite uhule nʼkudzaza ndi makhalidwe otayirira.+
29 Musamanyoze mwana wanu wamkazi pomupangitsa kuti akhale hule,+ kuopera kuti dziko lingachite uhule nʼkudzaza ndi makhalidwe otayirira.+