Levitiko 19:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Mlendo wokhala pakati panu muzimuona ngati mbadwa.+ Muzimukonda ngati mmene mumadzikondera nokha, chifukwa inunso munali alendo mʼdziko la Iguputo.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu. Levitiko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:34 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),12/2021, tsa. 12
34 Mlendo wokhala pakati panu muzimuona ngati mbadwa.+ Muzimukonda ngati mmene mumadzikondera nokha, chifukwa inunso munali alendo mʼdziko la Iguputo.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu.