Levitiko 19:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Musamachite chinyengo poyeza kutalika kwa chinthu, kulemera kwa chinthu kapena poyeza kuchuluka kwa zinthu.+ Levitiko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:35 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),12/2021, tsa. 10
35 Musamachite chinyengo poyeza kutalika kwa chinthu, kulemera kwa chinthu kapena poyeza kuchuluka kwa zinthu.+