Levitiko 20:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Uza Aisiraeli kuti, ‘Munthu aliyense wa Chiisiraeli ndiponso mlendo aliyense wokhala mu Isiraeli amene wapereka mwana wake aliyense kwa Moleki, aziphedwa ndithu.+ Nzika zamʼdziko lanu zizimupha pomuponya miyala.
2 “Uza Aisiraeli kuti, ‘Munthu aliyense wa Chiisiraeli ndiponso mlendo aliyense wokhala mu Isiraeli amene wapereka mwana wake aliyense kwa Moleki, aziphedwa ndithu.+ Nzika zamʼdziko lanu zizimupha pomuponya miyala.