Levitiko 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ine ndidzamukana munthu ameneyo ndipo ndidzamupha kuti asakhalenso pakati pa anthu a mtundu wake, chifukwa wapereka mwana wake kwa Moleki ndipo wadetsa malo anga oyera+ komanso waipitsa dzina langa loyera.
3 Ine ndidzamukana munthu ameneyo ndipo ndidzamupha kuti asakhalenso pakati pa anthu a mtundu wake, chifukwa wapereka mwana wake kwa Moleki ndipo wadetsa malo anga oyera+ komanso waipitsa dzina langa loyera.