Levitiko 20:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 ineyo ndidzadana ndi munthu ameneyo limodzi ndi banja lake.+ Ndidzapha munthu ameneyu limodzi ndi onse ogwirizana naye pochita uhule ndi Moleki, kuti asakhalenso pakati pa anthu awo.
5 ineyo ndidzadana ndi munthu ameneyo limodzi ndi banja lake.+ Ndidzapha munthu ameneyu limodzi ndi onse ogwirizana naye pochita uhule ndi Moleki, kuti asakhalenso pakati pa anthu awo.