Levitiko 20:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho mudzipatule ndipo mukhale oyera,+ chifukwa ine ndine Yehova Mulungu wanu.