Levitiko 20:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Muzisunga malamulo anga ndipo muziwatsatira.+ Ine ndine Yehova amene ndikukupatulani kuti mukhale oyera.+
8 Muzisunga malamulo anga ndipo muziwatsatira.+ Ine ndine Yehova amene ndikukupatulani kuti mukhale oyera.+