Levitiko 20:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Munthu akatemberera* bambo kapena mayi ake, aziphedwa ndithu.+ Mlandu wa magazi ake ukhale pa iye chifukwa watemberera bambo ake kapena mayi ake. Levitiko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:9 Nsanja ya Olonda,5/15/2004, tsa. 24
9 Munthu akatemberera* bambo kapena mayi ake, aziphedwa ndithu.+ Mlandu wa magazi ake ukhale pa iye chifukwa watemberera bambo ake kapena mayi ake.