Levitiko 20:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ili ndi lamulo lokhudza munthu amene wachita chigololo ndi mkazi wa munthu wina: Mwamuna amene wachita chigololo ndi mkazi wa mwiniwake aziphedwa ndithu. Mwamuna ndi mkazi amene achita chigololowo onse aziphedwa.+
10 Ili ndi lamulo lokhudza munthu amene wachita chigololo ndi mkazi wa munthu wina: Mwamuna amene wachita chigololo ndi mkazi wa mwiniwake aziphedwa ndithu. Mwamuna ndi mkazi amene achita chigololowo onse aziphedwa.+