Levitiko 20:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mwamuna amene wagona ndi mkazi wa bambo ake, wachititsa manyazi* bambo akewo.+ Mwamuna ndi mkaziyo aziphedwa ndithu. Mlandu wa magazi awo uzikhala pa iwo.
11 Mwamuna amene wagona ndi mkazi wa bambo ake, wachititsa manyazi* bambo akewo.+ Mwamuna ndi mkaziyo aziphedwa ndithu. Mlandu wa magazi awo uzikhala pa iwo.