Levitiko 20:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mwamuna akagona ndi mpongozi wake wamkazi, onse awiri aziphedwa ndithu. Iwo achita zinthu zosemphana ndi chibadwa. Mlandu wa magazi awo uzikhala pa iwo.+
12 Mwamuna akagona ndi mpongozi wake wamkazi, onse awiri aziphedwa ndithu. Iwo achita zinthu zosemphana ndi chibadwa. Mlandu wa magazi awo uzikhala pa iwo.+