Levitiko 20:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mwamuna akagona ndi mwamuna mnzake ngati mmene mwamuna amagonera ndi mkazi, onse awiri achita chinthu chonyansa.+ Iwo aziphedwa ndithu. Mlandu wa magazi awo uzikhala pa iwo.
13 Mwamuna akagona ndi mwamuna mnzake ngati mmene mwamuna amagonera ndi mkazi, onse awiri achita chinthu chonyansa.+ Iwo aziphedwa ndithu. Mlandu wa magazi awo uzikhala pa iwo.