Levitiko 20:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mwamuna akakwatira mkazi nʼkugonanso ndi mayi a mkaziyo, limenelo ndi khalidwe lonyansa.*+ Mwamunayo ndi akazi onsewo* aziphedwa kenako nʼkuwawotcha+ kuti anthu asapitirize kuchita khalidwe lonyansalo.
14 Mwamuna akakwatira mkazi nʼkugonanso ndi mayi a mkaziyo, limenelo ndi khalidwe lonyansa.*+ Mwamunayo ndi akazi onsewo* aziphedwa kenako nʼkuwawotcha+ kuti anthu asapitirize kuchita khalidwe lonyansalo.