Levitiko 20:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndipo mwamuna amene wagona ndi mkazi wa mchimwene wa bambo ake, wachititsa manyazi* mchimwene wa bambo akewo.+ Mwamuna ndi mkaziyo aziyankha mlandu wa tchimo lawolo. Iwo ayenera kufa kuti asabereke ana.
20 Ndipo mwamuna amene wagona ndi mkazi wa mchimwene wa bambo ake, wachititsa manyazi* mchimwene wa bambo akewo.+ Mwamuna ndi mkaziyo aziyankha mlandu wa tchimo lawolo. Iwo ayenera kufa kuti asabereke ana.