Levitiko 20:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mwamuna akakwatira mkazi wa mchimwene wake, wachita chinthu chonyansa.+ Iye wachititsa manyazi* mchimwene wake. Mwamuna ndi mkaziyo ayenera kufa kuti asabereke ana.
21 Mwamuna akakwatira mkazi wa mchimwene wake, wachita chinthu chonyansa.+ Iye wachititsa manyazi* mchimwene wake. Mwamuna ndi mkaziyo ayenera kufa kuti asabereke ana.