Levitiko 20:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Musamatsatire malamulo a mitundu imene ndikuithamangitsa pamaso panu,+ chifukwa iwo amachita zonsezi ndipo amandinyansa.+
23 Musamatsatire malamulo a mitundu imene ndikuithamangitsa pamaso panu,+ chifukwa iwo amachita zonsezi ndipo amandinyansa.+