Levitiko 20:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Muzisiyanitsa nyama yoyera ndi yodetsedwa, mbalame yodetsedwa ndi yoyera.+ Musadziipitse ndi nyama, mbalame kapena chilichonse chokwawa padziko lapansi chimene ndanena kuti ndi chodetsedwa.+
25 Muzisiyanitsa nyama yoyera ndi yodetsedwa, mbalame yodetsedwa ndi yoyera.+ Musadziipitse ndi nyama, mbalame kapena chilichonse chokwawa padziko lapansi chimene ndanena kuti ndi chodetsedwa.+