Levitiko 20:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Mwamuna kapena mkazi aliyense amene amalankhula ndi mizimu kapena kulosera zamʼtsogolo* aziphedwa ndithu.+ Aziphedwa powaponya miyala. Mlandu wa magazi awo uzikhala pa iwo.’”
27 Mwamuna kapena mkazi aliyense amene amalankhula ndi mizimu kapena kulosera zamʼtsogolo* aziphedwa ndithu.+ Aziphedwa powaponya miyala. Mlandu wa magazi awo uzikhala pa iwo.’”