Levitiko 21:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Asamatuluke mʼmalo opatulika ndipo asamadetse malo opatulika a Mulungu wake,+ chifukwa pamutu pake pali chizindikiro cha kudzipereka, chomwe ndi mafuta odzozera a Mulungu wake.+ Ine ndine Yehova.
12 Asamatuluke mʼmalo opatulika ndipo asamadetse malo opatulika a Mulungu wake,+ chifukwa pamutu pake pali chizindikiro cha kudzipereka, chomwe ndi mafuta odzozera a Mulungu wake.+ Ine ndine Yehova.