Levitiko 21:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Lankhula ndi Aroni kuti, ‘Munthu aliyense mwa ana ako,* ku mibadwo yawo yonse, amene ali ndi chilema asayandikire malo opatulika kudzapereka chakudya cha Mulungu wake.
17 “Lankhula ndi Aroni kuti, ‘Munthu aliyense mwa ana ako,* ku mibadwo yawo yonse, amene ali ndi chilema asayandikire malo opatulika kudzapereka chakudya cha Mulungu wake.