Levitiko 21:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 wa linunda, wamfupi kwambiri,* wa diso lolumala, wa zikanga, wa zipere ndi wa mavalo owonongeka.+