Levitiko 21:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Munthu aliyense mwa ana a Aroni* wansembe, amene ali ndi chilema, asamayandikire guwa lansembe kudzapereka nsembe yowotcha pamoto kwa Yehova. Asamayandikire guwa lansembe kudzapereka chakudya cha Mulungu wake chifukwa ali ndi chilema.
21 Munthu aliyense mwa ana a Aroni* wansembe, amene ali ndi chilema, asamayandikire guwa lansembe kudzapereka nsembe yowotcha pamoto kwa Yehova. Asamayandikire guwa lansembe kudzapereka chakudya cha Mulungu wake chifukwa ali ndi chilema.