Levitiko 22:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Uwauze kuti, ‘Mʼmibadwo yanu yonse munthu aliyense wodetsedwa mwa ana anu, amene wakhudza zinthu zopatulika zimene Aisiraeli azipatula kuti azipereke nsembe kwa Yehova, munthu ameneyo aziphedwa kuti asakhalenso pamaso panga.+ Ine ndine Yehova.
3 Uwauze kuti, ‘Mʼmibadwo yanu yonse munthu aliyense wodetsedwa mwa ana anu, amene wakhudza zinthu zopatulika zimene Aisiraeli azipatula kuti azipereke nsembe kwa Yehova, munthu ameneyo aziphedwa kuti asakhalenso pamaso panga.+ Ine ndine Yehova.