Levitiko 22:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Dzuwa likalowa adzakhalanso woyera, ndipo pambuyo pake akhoza kudya zina mwa zinthu zopatulika, chifukwa ndi chakudya chake.+
7 Dzuwa likalowa adzakhalanso woyera, ndipo pambuyo pake akhoza kudya zina mwa zinthu zopatulika, chifukwa ndi chakudya chake.+