Levitiko 22:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Sakuyeneranso kudya nyama iliyonse imene waipeza yakufa kapena imene yaphedwa ndi zilombo nʼkukhala wodetsedwa.+ Ine ndine Yehova.
8 Sakuyeneranso kudya nyama iliyonse imene waipeza yakufa kapena imene yaphedwa ndi zilombo nʼkukhala wodetsedwa.+ Ine ndine Yehova.