Levitiko 22:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Munthu wamba* asadye chinthu chopatulika chilichonse.+ Mlendo wokhala mʼnyumba ya wansembe kapena munthu waganyu, asadye chinthu chopatulika chilichonse.
10 Munthu wamba* asadye chinthu chopatulika chilichonse.+ Mlendo wokhala mʼnyumba ya wansembe kapena munthu waganyu, asadye chinthu chopatulika chilichonse.