Levitiko 22:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma mwana wa wansembe akakhala mkazi wamasiye kapena ngati anasiyidwa ukwati alibe mwana aliyense, ndipo wabwerera kunyumba kwa bambo ake kumene anali ali mwana, angathe kudya nawo chakudya cha bambo ake.+ Koma munthu wamba* asamadye nawo.
13 Koma mwana wa wansembe akakhala mkazi wamasiye kapena ngati anasiyidwa ukwati alibe mwana aliyense, ndipo wabwerera kunyumba kwa bambo ake kumene anali ali mwana, angathe kudya nawo chakudya cha bambo ake.+ Koma munthu wamba* asamadye nawo.