Levitiko 22:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Munthu akadya mosadziwa chinthu chopatulika, azibweza chinthucho nʼkuwonjezerapo gawo limodzi mwa magawo 5 a chinthucho. Azipereka chinthu chopatulikacho kwa wansembe.+
14 Munthu akadya mosadziwa chinthu chopatulika, azibweza chinthucho nʼkuwonjezerapo gawo limodzi mwa magawo 5 a chinthucho. Azipereka chinthu chopatulikacho kwa wansembe.+