Levitiko 22:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ngati munthu akupereka nsembe yamgwirizano+ kwa Yehova kuti akwaniritse lonjezo lake kapena kuti ikhale nsembe yaufulu, azipereka ngʼombe kapena nkhosa yopanda chilema, kuti Mulungu ailandire. Izikhala yopanda chilema chilichonse. Levitiko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:21 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),2/2019, tsa. 3
21 Ngati munthu akupereka nsembe yamgwirizano+ kwa Yehova kuti akwaniritse lonjezo lake kapena kuti ikhale nsembe yaufulu, azipereka ngʼombe kapena nkhosa yopanda chilema, kuti Mulungu ailandire. Izikhala yopanda chilema chilichonse.