-
Levitiko 22:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Musamapereke kwa Yehova nyama imene mavalo ake ndi owonongeka, ophwanyika kapena yofulidwa. Musamapereke nsembe nyama zoterezi mʼdziko lanu.
-