-
Levitiko 22:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Ndipo nyama iliyonse mwa nyama zoterezi imene mlendo wakupatsani musamaipereke nsembe kuti ikhale chakudya cha Mulungu wanu, chifukwa ili ndi chilema ndipo Mulungu sadzailandira.’”
-