Levitiko 22:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 “Ngʼombe, nkhosa kapena mbuzi ikabadwa, izikhala ndi mayi ake masiku 7,+ koma kuyambira tsiku la 8 kupita mʼtsogolo mungaipereke kwa Yehova monga nsembe yowotcha pamoto, ndipo Mulungu adzailandira.
27 “Ngʼombe, nkhosa kapena mbuzi ikabadwa, izikhala ndi mayi ake masiku 7,+ koma kuyambira tsiku la 8 kupita mʼtsogolo mungaipereke kwa Yehova monga nsembe yowotcha pamoto, ndipo Mulungu adzailandira.