Levitiko 22:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mukafuna kupereka nsembe yoyamikira kwa Yehova+ muziipereka mʼnjira yakuti Mulungu asangalale nanu.
29 Mukafuna kupereka nsembe yoyamikira kwa Yehova+ muziipereka mʼnjira yakuti Mulungu asangalale nanu.