Levitiko 23:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Uza Aisiraeli kuti, ‘Mukadzalowa mʼdziko limene ndikukupatsani, nʼkukolola mbewu zamʼdzikomo, muzidzabweretsa kwa wansembe+ mtolo umodzi wa zipatso zanu zoyambirira.+ Levitiko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:10 Nsanja ya Olonda,7/15/2007, tsa. 26
10 “Uza Aisiraeli kuti, ‘Mukadzalowa mʼdziko limene ndikukupatsani, nʼkukolola mbewu zamʼdzikomo, muzidzabweretsa kwa wansembe+ mtolo umodzi wa zipatso zanu zoyambirira.+