-
Levitiko 23:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Ndipo wansembe azidzayendetsa mtolowo uku ndi uku pamaso pa Yehova kuti Mulungu asangalale nanu. Sabata likatha, wansembe azidzayendetsa mtolowo uku ndi uku pa tsiku lotsatira.
-