Levitiko 23:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Muziwerenga masiku 50+ kukafika pa tsiku lotsatizana ndi tsiku limene Sabata la 7 lathera, kenako muzipereka nsembe yambewu zatsopano kwa Yehova.+
16 Muziwerenga masiku 50+ kukafika pa tsiku lotsatizana ndi tsiku limene Sabata la 7 lathera, kenako muzipereka nsembe yambewu zatsopano kwa Yehova.+