Levitiko 23:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pa tsiku limeneli muzilengeza+ kuti kuli msonkhano wopatulika ndipo musamagwire ntchito iliyonse yotopetsa. Limeneli ndi lamulo mpaka kalekale kulikonse kumene mungakhale mʼmibadwo yanu yonse.
21 Pa tsiku limeneli muzilengeza+ kuti kuli msonkhano wopatulika ndipo musamagwire ntchito iliyonse yotopetsa. Limeneli ndi lamulo mpaka kalekale kulikonse kumene mungakhale mʼmibadwo yanu yonse.