Levitiko 23:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mukamakolola zinthu zamʼmunda mwanu, musamachotseretu zonse mʼmphepete mwa mundawo, ndipo musamachite khunkha mʼmunda mwanumo.+ Zotsalazo muzisiyira wosauka*+ ndi mlendo wokhala pakati panu.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu.’”
22 Mukamakolola zinthu zamʼmunda mwanu, musamachotseretu zonse mʼmphepete mwa mundawo, ndipo musamachite khunkha mʼmunda mwanumo.+ Zotsalazo muzisiyira wosauka*+ ndi mlendo wokhala pakati panu.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu.’”