Levitiko 23:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Muzichita zimenezi kuwonjezera pa zimene mumapereka pa masabata a Yehova,+ mphatso zanu,+ nsembe zanu zimene mumapereka pokwaniritsa lonjezo+ ndi nsembe zanu zonse zaufulu+ zimene mukuyenera kupereka kwa Yehova.
38 Muzichita zimenezi kuwonjezera pa zimene mumapereka pa masabata a Yehova,+ mphatso zanu,+ nsembe zanu zimene mumapereka pokwaniritsa lonjezo+ ndi nsembe zanu zonse zaufulu+ zimene mukuyenera kupereka kwa Yehova.