Levitiko 24:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Nyalezo azikhazike pachoikapo nyale+ chagolide woyenga bwino, ndipo zizikhala pamaso pa Yehova nthawi zonse.
4 Nyalezo azikhazike pachoikapo nyale+ chagolide woyenga bwino, ndipo zizikhala pamaso pa Yehova nthawi zonse.