Levitiko 24:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Utenge ufa wosalala nʼkuphika mikate 12 yozungulira yoboola pakati. Mkate uliwonse uzipangidwa ndi ufa wokwanira magawo awiri mwa magawo 10 a muyezo wa efa.*
5 Utenge ufa wosalala nʼkuphika mikate 12 yozungulira yoboola pakati. Mkate uliwonse uzipangidwa ndi ufa wokwanira magawo awiri mwa magawo 10 a muyezo wa efa.*