Levitiko 24:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mkatewo uzikhala wa Aroni ndi ana ake,+ ndipo aziudyera mʼmalo oyera,+ chifukwa waperekedwa kwa iye monga chinthu choyera koposa kuchokera pa nsembe zowotcha pamoto zoperekedwa kwa Yehova. Limeneli likhale lamulo mpaka kalekale.”
9 Mkatewo uzikhala wa Aroni ndi ana ake,+ ndipo aziudyera mʼmalo oyera,+ chifukwa waperekedwa kwa iye monga chinthu choyera koposa kuchokera pa nsembe zowotcha pamoto zoperekedwa kwa Yehova. Limeneli likhale lamulo mpaka kalekale.”