Levitiko 24:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Munthu wotemberera dzina la Mulungu uja, mupite naye kunja kwa msasa. Onse amene anamumva akutemberera aike manja awo pamutu pake ndipo gulu lonse limuponye miyala.+
14 “Munthu wotemberera dzina la Mulungu uja, mupite naye kunja kwa msasa. Onse amene anamumva akutemberera aike manja awo pamutu pake ndipo gulu lonse limuponye miyala.+