Levitiko 24:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Munthu akavulaza mnzake, zimene wachitira mnzakezo iyenso muzimʼchitira zomwezo.+