Levitiko 24:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kuthyola fupa kulipira kuthyola fupa, diso kulipira diso, dzino kulipira dzino. Mmene wavulazira mnzake nayenso muzimʼvulaza chimodzimodzi.+ Levitiko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:20 Galamukani!,9/2010, ptsa. 10-11 Nsanja ya Olonda,9/1/2009, tsa. 22
20 Kuthyola fupa kulipira kuthyola fupa, diso kulipira diso, dzino kulipira dzino. Mmene wavulazira mnzake nayenso muzimʼvulaza chimodzimodzi.+