Levitiko 25:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Uza Aisiraeli kuti, ‘Mukakalowa mʼdziko limene ndikukupatsani,+ dzikolo lizikasunga sabata la Yehova.+
2 “Uza Aisiraeli kuti, ‘Mukakalowa mʼdziko limene ndikukupatsani,+ dzikolo lizikasunga sabata la Yehova.+