-
Levitiko 25:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Koma mungathe kudya chakudya chimene chamera mʼmunda mwanu mʼchaka cha sabatacho. Inuyo, kapolo wanu wamwamuna, kapolo wanu wamkazi, waganyu wanu ndi alendo amene akukhala mʼnyumba mwanu mungathe kudya.
-